2 Mbiri 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atsogoleri amenewa ankayangʼanira asilikali okwana 307,500, okonzeka kumenya nkhondo. Limeneli linali gulu lamphamvu la asilikali lomwe linkathandiza mfumu kulimbana ndi adani.+
13 Atsogoleri amenewa ankayangʼanira asilikali okwana 307,500, okonzeka kumenya nkhondo. Limeneli linali gulu lamphamvu la asilikali lomwe linkathandiza mfumu kulimbana ndi adani.+