2 Mbiri 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Uziya, amene anali atanyamula choperekera nsembe, anawakwiyira kwambiri+ ansembewo. Zitatero, anachita khate+ pachipumi pake. Anachita khatelo ansembewo ali pompo mʼnyumba ya Yehova pafupi ndi guwa lansembe zofukiza. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2144
19 Koma Uziya, amene anali atanyamula choperekera nsembe, anawakwiyira kwambiri+ ansembewo. Zitatero, anachita khate+ pachipumi pake. Anachita khatelo ansembewo ali pompo mʼnyumba ya Yehova pafupi ndi guwa lansembe zofukiza.