-
2 Mbiri 26:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Wansembe wamkulu Azariya ndi ansembe ena onse atamuyangʼana, anangoona kuti wachita khate pachipumi. Choncho anayamba kumutulutsa msangamsanga ndipo mwiniwakeyonso anatuluka mofulumira chifukwa Yehova anali atamuchititsa khate.
-