2 Mbiri 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso Aisiraeli anagwira abale awo okwana 200,000 nʼkuwatenga. Pa anthu ogwidwawo panali azimayi komanso ana aamuna ndi aakazi. Anatenganso zinthu zawo zambiri nʼkupita nazo ku Samariya.+
8 Komanso Aisiraeli anagwira abale awo okwana 200,000 nʼkuwatenga. Pa anthu ogwidwawo panali azimayi komanso ana aamuna ndi aakazi. Anatenganso zinthu zawo zambiri nʼkupita nazo ku Samariya.+