2 Mbiri 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano mukufuna kuti anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu akhale antchito anu aamuna ndi aakazi.+ Kodi mʼmesa inunso muli ndi mlandu kwa Yehova Mulungu wanu?
10 Tsopano mukufuna kuti anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu akhale antchito anu aamuna ndi aakazi.+ Kodi mʼmesa inunso muli ndi mlandu kwa Yehova Mulungu wanu?