-
2 Mbiri 28:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Zitatero, amuna ena omwe anali atsogoleri a anthu a fuko la Efuraimu omwe ndi Azariya mwana wa Yehohanani, Berekiya mwana wa Mesilemoti, Yehizikiya mwana wa Salumu ndi Amasa mwana wa Hadilai anadzudzula asilikali amene anabwera kuchokera kunkhondowo.
-