-
2 Mbiri 28:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Iwo anawauza kuti: “Musabweretse kuno anthu amene mwawagwirawo chifukwa tikhala ndi mlandu kwa Yehova. Zimene mukufuna kuchitazi, ziwonjezera machimo athu ndiponso mlandu wathu. Tili kale ndi mlandu waukulu, ndipo Mulungu wakwiyira kwambiri Isiraeli.”
-