2 Mbiri 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho asilikaliwo anasiya anthu aja ndiponso zinthu zimene anatenga+ zija mʼmanja mwa akalonga ndi anthu onse amene anasonkhana pamenepo.
14 Choncho asilikaliwo anasiya anthu aja ndiponso zinthu zimene anatenga+ zija mʼmanja mwa akalonga ndi anthu onse amene anasonkhana pamenepo.