2 Mbiri 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yehova anakwiyira kwambiri anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu+ ndipo anawabweretsera tsoka kuti anthu owaona komanso kumva za tsokalo azichita mantha, kudabwa ndiponso kuwaimbira mluzu, ngati mmene mukuonera ndi maso anu.+
8 Choncho Yehova anakwiyira kwambiri anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu+ ndipo anawabweretsera tsoka kuti anthu owaona komanso kumva za tsokalo azichita mantha, kudabwa ndiponso kuwaimbira mluzu, ngati mmene mukuonera ndi maso anu.+