2 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno inu ana anga, ino ndi nthawi yochita zinthu mwamphamvu, chifukwa Yehova wakusankhani kuti muziima pamaso pake nʼkumamutumikira+ ndiponso kuti muzipereka nsembe zautsi.”+
11 Ndiyeno inu ana anga, ino ndi nthawi yochita zinthu mwamphamvu, chifukwa Yehova wakusankhani kuti muziima pamaso pake nʼkumamutumikira+ ndiponso kuti muzipereka nsembe zautsi.”+