2 Mbiri 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ansembe analowa mʼnyumba ya Yehova kukayeretsamo, ndipo anatulutsa zonyansa zonse zimene anazipeza mʼkachisi wa Yehova nʼkupita nazo pabwalo+ la nyumba ya Yehova. Ndiyeno Alevi anazitenga nʼkupita nazo kunja kuchigwa cha Kidironi.+
16 Kenako ansembe analowa mʼnyumba ya Yehova kukayeretsamo, ndipo anatulutsa zonyansa zonse zimene anazipeza mʼkachisi wa Yehova nʼkupita nazo pabwalo+ la nyumba ya Yehova. Ndiyeno Alevi anazitenga nʼkupita nazo kunja kuchigwa cha Kidironi.+