2 Mbiri 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anayamba kuyeretsa pa tsiku loyamba la mwezi woyamba ndipo pa tsiku la 8 la mweziwo anafika pakhonde la nyumba ya Yehova.+ Anayeretsa nyumba ya Yehovayo masiku 8 ndipo pa tsiku la 16 la mwezi woyamba anamaliza ntchitoyo.
17 Anayamba kuyeretsa pa tsiku loyamba la mwezi woyamba ndipo pa tsiku la 8 la mweziwo anafika pakhonde la nyumba ya Yehova.+ Anayeretsa nyumba ya Yehovayo masiku 8 ndipo pa tsiku la 16 la mwezi woyamba anamaliza ntchitoyo.