2 Mbiri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ziwiya zonse zimene Mfumu Ahazi anasiya kuzigwiritsira ntchito mu ulamuliro wake pamene ankachita zosakhulupirika,+ tazikonza nʼkuziyeretsa+ ndipo zili pafupi ndi guwa lansembe la Yehova.”
19 Ziwiya zonse zimene Mfumu Ahazi anasiya kuzigwiritsira ntchito mu ulamuliro wake pamene ankachita zosakhulupirika,+ tazikonza nʼkuziyeretsa+ ndipo zili pafupi ndi guwa lansembe la Yehova.”