-
2 Mbiri 29:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kenako anabweretsa mbuzi zamphongo za nsembe yamachimo zija pafupi ndi mfumu ndi gulu lonse la anthu ndipo iwo anaika manja awo pambuzizo.
-