2 Mbiri 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Hezekiya analamula kuti apereke nsembe yopsereza paguwa lansembe.+ Atayamba kupereka nsembeyo, anayamba kuimba nyimbo ya Yehova ndiponso malipenga motsatira zipangizo zoimbira za Davide mfumu ya Isiraeli.
27 Kenako Hezekiya analamula kuti apereke nsembe yopsereza paguwa lansembe.+ Atayamba kupereka nsembeyo, anayamba kuimba nyimbo ya Yehova ndiponso malipenga motsatira zipangizo zoimbira za Davide mfumu ya Isiraeli.