-
2 Mbiri 29:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Gulu lonse la anthulo linagwada nʼkuwerama pamene nyimboyo inkaimbidwa ndiponso pamene malipenga ankaimbidwa. Ndipo zonsezi zinapitirira mpaka anamaliza kupereka nsembe yopsereza.
-