2 Mbiri 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno mfumu Hezekiya ndi akalonga anauza Alevi kuti atamande Yehova ndi mawu a Davide+ komanso a wamasomphenya Asafu.+ Choncho iwo anatamanda Mulungu mosangalala ndipo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo kufika pansi.
30 Ndiyeno mfumu Hezekiya ndi akalonga anauza Alevi kuti atamande Yehova ndi mawu a Davide+ komanso a wamasomphenya Asafu.+ Choncho iwo anatamanda Mulungu mosangalala ndipo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo kufika pansi.