-
2 Mbiri 30:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno asilikali othamanga amene anatenga makalata ochokera kwa mfumu ndi kwa akalonga ake, anapita mu Isiraeli ndi mu Yuda monse chifukwa mfumu inalamula kuti: “Inu Aisiraeli, bwererani kwa Yehova Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli, kuti iye abwerere kwa anthu amene anatsala, omwe anapulumuka mʼmanja mwa mafumu a Asuri.+
-