2 Mbiri 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakhale ngati makolo anu ndi abale anu amene anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wa makolo awo, moti anawachititsa kukhala chinthu chodabwitsa ngati mmene mukuoneramu.+
7 Musakhale ngati makolo anu ndi abale anu amene anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wa makolo awo, moti anawachititsa kukhala chinthu chodabwitsa ngati mmene mukuoneramu.+