2 Mbiri 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye musakhale ankhutukumve ngati makolo anu.+ Gonjerani Yehova ndipo mupite kunyumba yake yopatulika+ imene waiyeretsa mpaka kalekale. Tumikirani Yehova Mulungu wanu kuti asiye kukukwiyirani kwambiri.+
8 Ndiye musakhale ankhutukumve ngati makolo anu.+ Gonjerani Yehova ndipo mupite kunyumba yake yopatulika+ imene waiyeretsa mpaka kalekale. Tumikirani Yehova Mulungu wanu kuti asiye kukukwiyirani kwambiri.+