2 Mbiri 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ambirimbiri anasonkhana ku Yerusalemu kuti achite Chikondwerero cha Mkate Wopanda Zofufumitsa+ mʼmwezi wachiwiri+ ndipo linali gulu lalikulu kwambiri.
13 Anthu ambirimbiri anasonkhana ku Yerusalemu kuti achite Chikondwerero cha Mkate Wopanda Zofufumitsa+ mʼmwezi wachiwiri+ ndipo linali gulu lalikulu kwambiri.