2 Mbiri 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Aisiraeli amene anali ku Yerusalemu anachita Chikondwerero cha Mkate Wopanda Zofufumitsa+ mosangalala kwambiri kwa masiku 7.+ Alevi ndi ansembe ankatamanda Yehova tsiku ndi tsiku nʼkumaimbira Yehova mokweza ndi zipangizo zawo.+
21 Choncho Aisiraeli amene anali ku Yerusalemu anachita Chikondwerero cha Mkate Wopanda Zofufumitsa+ mosangalala kwambiri kwa masiku 7.+ Alevi ndi ansembe ankatamanda Yehova tsiku ndi tsiku nʼkumaimbira Yehova mokweza ndi zipangizo zawo.+