2 Mbiri 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno gulu lonse la anthulo linagwirizana kuti lichitenso phwando masiku ena 7. Choncho anachita phwandolo mosangalala masiku enanso 7.+
23 Ndiyeno gulu lonse la anthulo linagwirizana kuti lichitenso phwando masiku ena 7. Choncho anachita phwandolo mosangalala masiku enanso 7.+