2 Mbiri 30:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho anthu anasangalala kwambiri ku Yerusalemu, chifukwa kuyambira mʼmasiku a Solomo mwana wa Davide mfumu ya Isiraeli, zinthu ngati zimenezi zinali zisanachitike ku Yerusalemu.+
26 Choncho anthu anasangalala kwambiri ku Yerusalemu, chifukwa kuyambira mʼmasiku a Solomo mwana wa Davide mfumu ya Isiraeli, zinthu ngati zimenezi zinali zisanachitike ku Yerusalemu.+