2 Mbiri 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pomaliza, Alevi omwe anali ansembe anaimirira nʼkudalitsa anthuwo.+ Mulungu anamva mawu awo ndipo pemphero lawo linafika kumwamba, kumalo oyera omwe iye amakhala.
27 Pomaliza, Alevi omwe anali ansembe anaimirira nʼkudalitsa anthuwo.+ Mulungu anamva mawu awo ndipo pemphero lawo linafika kumwamba, kumalo oyera omwe iye amakhala.