-
2 Mbiri 31:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kenako Hezekiya anasankha ansembe mogwirizana ndi magulu awo+ komanso Alevi mogwirizana ndi magulu awo.+ Gulu lililonse la ansembe ndiponso la Alevi analiika mogwirizana ndi utumiki wawo+ wokhudza nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Anawasankha kuti azitumikira Mulungu, kumuyamika ndiponso kumutamanda mʼmageti a kachisi wa Yehova.+
-