2 Mbiri 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aisiraeli atangomva zimenezi, anapereka zinthu zambiri zoyambirira kukolola monga mbewu, vinyo watsopano, mafuta,+ uchi ndi zokolola zonse zakumunda+ ndipo anapereka mowolowa manja chakhumi cha zinthu zonse.+
5 Aisiraeli atangomva zimenezi, anapereka zinthu zambiri zoyambirira kukolola monga mbewu, vinyo watsopano, mafuta,+ uchi ndi zokolola zonse zakumunda+ ndipo anapereka mowolowa manja chakhumi cha zinthu zonse.+