2 Mbiri 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anayamba kuunjika milu ya zoperekazo mʼmwezi wachitatu+ ndipo anamaliza mʼmwezi wa 7.+