2 Mbiri 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mndandanda wa mayina a ansembe potengera makolo awo unali wotsatira nyumba ya makolo awo+ ngati mmene unalili mndandanda wa mayina a Alevi azaka 20 kupita mʼtsogolo,+ mogwirizana ndi ntchito za magulu awo.+
17 Mndandanda wa mayina a ansembe potengera makolo awo unali wotsatira nyumba ya makolo awo+ ngati mmene unalili mndandanda wa mayina a Alevi azaka 20 kupita mʼtsogolo,+ mogwirizana ndi ntchito za magulu awo.+