-
2 Mbiri 31:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mndandandawo unali wa ana awo onse aangʼono, akazi awo ndiponso ana awo aamuna ndi aakazi komanso mbumba yawo yonse, popeza anadziyeretsa kuti achite utumiki wopatulika, pa ntchito imene ankagwira chifukwa cha kukhulupirika kwawo.
-