-
2 Mbiri 31:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Panalinso mndandanda wa mayina a ansembe, mbadwa za Aroni, amene ankakhala kumalo odyetserako ziweto ozungulira mizinda yawo.+ Mʼmizinda yonseyo, amuna anasankhidwa pochita kuwatchula mayina, kuti azipereka chakudya kwa mwamuna aliyense pakati pa ansembe ndiponso kwa aliyense amene anali pamndandanda wa mayina a Alevi motsatira makolo awo.
-