2 Mbiri 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa nʼkusintha mtima wake wodzikuza.+ Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu ndipo Yehova sanawasonyeze mkwiyo wake mʼmasiku a Hezekiya.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:26 Yesaya 1, tsa. 397
26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa nʼkusintha mtima wake wodzikuza.+ Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu ndipo Yehova sanawasonyeze mkwiyo wake mʼmasiku a Hezekiya.+