2 Mbiri 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nkhani zina zokhudza Hezekiya ndiponso mmene anasonyezera chikondi chokhulupirika,+ zinalembedwa mʼmasomphenya a mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi omwe ali mʼBuku la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.+
32 Nkhani zina zokhudza Hezekiya ndiponso mmene anasonyezera chikondi chokhulupirika,+ zinalembedwa mʼmasomphenya a mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi omwe ali mʼBuku la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.+