2 Mbiri 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Manase bambo ake.+ Amoni ankapereka nsembe kwa zifaniziro zonse zogoba zimene bambo ake anapanga+ ndipo anapitiriza kuzitumikira.
22 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Manase bambo ake.+ Amoni ankapereka nsembe kwa zifaniziro zonse zogoba zimene bambo ake anapanga+ ndipo anapitiriza kuzitumikira.