-
2 Mbiri 34:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iwo anapita kwa Hilikiya mkulu wa ansembe nʼkumupatsa ndalama zimene anthu ankabweretsa kunyumba ya Mulungu, zimene Alevi omwe anali alonda apakhomo, anatolera kwa anthu a fuko la Manase, la Efuraimu, kwa Aisiraeli onse,+ kwa Ayuda onse, anthu a fuko la Benjamini ndiponso kwa anthu onse okhala ku Yerusalemu.
-