2 Mbiri 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ogwira ntchitowa anapereka ndalamazo kwa amisiri ndi kwa omanga nyumba kuti agulire miyala yosema komanso matabwa olimbitsira nyumba ndiponso kuti akhome mitanda ya nyumba zimene mafumu a Yuda anazilekerera kuti ziwonongeke.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:11 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 55
11 Anthu ogwira ntchitowa anapereka ndalamazo kwa amisiri ndi kwa omanga nyumba kuti agulire miyala yosema komanso matabwa olimbitsira nyumba ndiponso kuti akhome mitanda ya nyumba zimene mafumu a Yuda anazilekerera kuti ziwonongeke.+