2 Mbiri 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthuwo anagwira ntchitoyo mokhulupirika.+ Amene ankawayangʼanira anali Yahati ndi Obadiya, Alevi omwe anali mbadwa za Merari+ ndiponso Zekariya ndi Mesulamu mbadwa za Kohati.+ Aliyense wa Aleviwo, anali katswiri woimba+
12 Anthuwo anagwira ntchitoyo mokhulupirika.+ Amene ankawayangʼanira anali Yahati ndi Obadiya, Alevi omwe anali mbadwa za Merari+ ndiponso Zekariya ndi Mesulamu mbadwa za Kohati.+ Aliyense wa Aleviwo, anali katswiri woimba+