2 Mbiri 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ndipo ankayangʼanira anthu onyamula katundu ndi anthu onse ogwira ntchito zosiyanasiyana. Panalinso Alevi amene anali alembi, akapitawo ndi alonda apageti.+
13 ndipo ankayangʼanira anthu onyamula katundu ndi anthu onse ogwira ntchito zosiyanasiyana. Panalinso Alevi amene anali alembi, akapitawo ndi alonda apageti.+