-
2 Mbiri 34:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho Hilikiya anauza Safani mlembi kuti: “Ndapeza buku la Chilamulo mʼnyumba ya Yehova!” Atatero Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani.
-