2 Mbiri 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nʼchifukwa chake ndidzakuika mʼmanda a makolo ako ndipo udzaikidwa mʼmanda ako mwamtendere. Maso ako sadzaona tsoka lonse lomwe ndidzabweretse pamalo ano ndi anthu ake.’”’”+ Kenako iwo anakauza mfumuyo zimenezi.
28 Nʼchifukwa chake ndidzakuika mʼmanda a makolo ako ndipo udzaikidwa mʼmanda ako mwamtendere. Maso ako sadzaona tsoka lonse lomwe ndidzabweretse pamalo ano ndi anthu ake.’”’”+ Kenako iwo anakauza mfumuyo zimenezi.