2 Mbiri 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muphe nyama ya nsembe ya Pasika+ nʼkudziyeretsa ndipo muwakonzere abale anu nyama kuti mutsatire mawu a Yehova kudzera mwa Mose.”
6 Muphe nyama ya nsembe ya Pasika+ nʼkudziyeretsa ndipo muwakonzere abale anu nyama kuti mutsatire mawu a Yehova kudzera mwa Mose.”