2 Mbiri 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo atamaliza kukonzekera, ansembe anaimirira mʼmalo awo, komanso Alevi anali mʼmagulu awo+ mogwirizana ndi zimene mfumu inalamula.
10 Iwo atamaliza kukonzekera, ansembe anaimirira mʼmalo awo, komanso Alevi anali mʼmagulu awo+ mogwirizana ndi zimene mfumu inalamula.