2 Mbiri 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero anapha nyama ya Pasika+ ndipo ansembe anawaza paguwa lansembe magazi amene anapatsidwa.+ Pa nthawiyi nʼkuti Alevi akusenda nyamazo.+
11 Atatero anapha nyama ya Pasika+ ndipo ansembe anawaza paguwa lansembe magazi amene anapatsidwa.+ Pa nthawiyi nʼkuti Alevi akusenda nyamazo.+