-
2 Mbiri 35:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pambuyo pake anakonza nyama yawo ndi ya ansembe chifukwa ansembe, mbadwa za Aroni, ankapereka nsembe zopsereza ndiponso nsembe za mafuta mpaka kunja kunada. Choncho Alevi anakonza nyama yawo ndi ya ansembe, mbadwa za Aroni.
-