-
2 Mbiri 35:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Neko anatumiza anthu kuti akamuuze kuti: “Kodi chikukukhudza nʼchiyani iwe mfumu ya Yuda? Ulendo uno sindinabwere kudzamenyana ndi iwe. Ndabwera kudzamenyana ndi mtundu wina ndipo Mulungu wanena kuti ndisachedwe. Ngati ukufuna kuti zinthu zikuyendere bwino, usachite zimenezi. Usatsutsane ndi Mulungu amene ali ndi ine chifukwa akhoza kukuwononga.”
-