-
2 Mbiri 35:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kenako asilikali oponya mivi analasa Mfumu Yosiya. Choncho mfumuyo inauza atumiki ake kuti: “Ndichotseni malo ano chifukwa ndavulala kwambiri.”
-