2 Mbiri 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nkhani zina zokhudza Yehoyakimu, zonyansa zimene anachita ndiponso zoipa zimene zinapezeka zokhudza iyeyo, zinalembedwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda. Kenako mwana wake Yehoyakini anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
8 Nkhani zina zokhudza Yehoyakimu, zonyansa zimene anachita ndiponso zoipa zimene zinapezeka zokhudza iyeyo, zinalembedwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda. Kenako mwana wake Yehoyakini anakhala mfumu mʼmalo mwake.+