2 Mbiri 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake. Ndipo sanadzichepetse pamaso pa mneneri Yeremiya+ yemwe ankalankhula molamulidwa ndi Yehova.
12 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake. Ndipo sanadzichepetse pamaso pa mneneri Yeremiya+ yemwe ankalankhula molamulidwa ndi Yehova.