Ezara 2:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Choncho, bwanamkubwa* anawauza kuti asamadye zinthu zopatulika koposa,+ mpaka patakhala wansembe amene angagwiritse ntchito Urimu ndi Tumimu.+ Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:63 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 181/15/1986, tsa. 8
63 Choncho, bwanamkubwa* anawauza kuti asamadye zinthu zopatulika koposa,+ mpaka patakhala wansembe amene angagwiritse ntchito Urimu ndi Tumimu.+