Ezara 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano popeza ife timalandira malipiro ochokera kunyumba yachifumu,* si bwino kuti tingolekerera kuti inu mfumu chuma chanu chiwonongeke. Choncho, tatumiza kalatayi kuti tikudziwitseni zimenezi inu mfumu
14 Tsopano popeza ife timalandira malipiro ochokera kunyumba yachifumu,* si bwino kuti tingolekerera kuti inu mfumu chuma chanu chiwonongeke. Choncho, tatumiza kalatayi kuti tikudziwitseni zimenezi inu mfumu